Mateyu 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Iwe unditsatirebe ine, ndipo aleke akufa aike akufa awo.”+