Aheberi 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+
11 Mwa chikhulupiriro, Sara+ nayenso analandira mphamvu yokhala ndi pakati* ngakhale kuti anali atapitirira zaka zobereka,+ chifukwa anaona kuti wolonjezayo ndi wokhulupirika.+