Yesaya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuyambira kuphazi mpaka kumutu palibe pabwino.+ Thupi lanu lonse lili ndi mabala ndi zilonda, ndiponso lanyukanyuka. Palibe amene wafinya zilonda zanuzo kapena kuzimanga. Palibenso amene wazifewetsa ndi mafuta.+
6 Kuyambira kuphazi mpaka kumutu palibe pabwino.+ Thupi lanu lonse lili ndi mabala ndi zilonda, ndiponso lanyukanyuka. Palibe amene wafinya zilonda zanuzo kapena kuzimanga. Palibenso amene wazifewetsa ndi mafuta.+