Salimo 119:120 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+ Aheberi 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kulandira chilango chochokera kwa Mulungu wamoyo n’chinthu choopsa.+
120 Chifukwa choopa inu, thupi langa linagwidwa nthumanzi,+Ndipo chifukwa cha zigamulo zanu, ndinachita mantha.+