Ekisodo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho pita. Ine ndidzakhala nawe polankhula ndipo ndidzakuuza zonena.”+ Machitidwe 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo sanathe kulimbana ndi nzeru+ zimene anasonyeza komanso mzimu woyera umene unali kumutsogolera pamene anali kulankhula.+ 1 Petulo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chitani zimenezi pamene mukumutulira nkhawa zanu zonse,+ pakuti amakuderani nkhawa.+
10 Koma iwo sanathe kulimbana ndi nzeru+ zimene anasonyeza komanso mzimu woyera umene unali kumutsogolera pamene anali kulankhula.+