1 Mafumu 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumukazi ya ku Sheba itaona nzeru zonse za Solomo,+ nyumba imene anamanga,+ 2 Mbiri 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mfumukazi ya ku Sheba itaona nzeru za Solomo,+ nyumba imene anamanga,+ Mateyu 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komatu ndikukuuzani kuti ngakhale Solomo+ mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati lililonse la maluwa amenewa.
29 Komatu ndikukuuzani kuti ngakhale Solomo+ mu ulemerero wake wonse sanavalepo zokongola ngati lililonse la maluwa amenewa.