Mateyu 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ufumu wakumwamba udzakhala ngati anamwali 10 amene anatenga nyale+ zawo n’kupita kukachingamira mkwati.+ Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+
25 “Ufumu wakumwamba udzakhala ngati anamwali 10 amene anatenga nyale+ zawo n’kupita kukachingamira mkwati.+
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+