Luka 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Udzakondwa ndi kusangalala kwambiri, ndipo ambiri adzasangalala+ ndi kubadwa kwake Aroma 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sangalalani ndi anthu amene akusangalala.+ Lirani ndi anthu amene akulira.