Luka 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya, chifukwa pembedzero lako lamveka ndithu.+ Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna, ndipo udzamutche Yohane.+
13 Koma mngeloyo anamuuza kuti: “Usachite mantha Zekariya, chifukwa pembedzero lako lamveka ndithu.+ Mkazi wako Elizabeti adzakuberekera mwana wamwamuna, ndipo udzamutche Yohane.+