Mateyu 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Anawauzanso fanizo lina,+ kuti: “Ufumu wakumwamba uli ngati kanjere ka mpiru*+ kamene munthu anakatenga ndi kukabzala m’munda wake. Maliko 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye anapitiriza kuti: “Kodi ufumu wa Mulungu tingauyerekeze ndi chiyani? Kapena kodi tingaufotokoze ndi fanizo lotani?+
31 Anawauzanso fanizo lina,+ kuti: “Ufumu wakumwamba uli ngati kanjere ka mpiru*+ kamene munthu anakatenga ndi kukabzala m’munda wake.
30 Iye anapitiriza kuti: “Kodi ufumu wa Mulungu tingauyerekeze ndi chiyani? Kapena kodi tingaufotokoze ndi fanizo lotani?+