Mateyu 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mofanana ndi zimenezi, Atate wanga wakumwamba sakufuna kuti mmodzi wa tianati akawonongeke.+ Aroma 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sangalalani ndi anthu amene akusangalala.+ Lirani ndi anthu amene akulira. 1 Petulo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.
25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.