Mateyu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mbuye wakeyo anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe!+ Unakhulupirika+ pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti udziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’ Luka 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuuza kuti, ‘Unagwira ntchito, ndiwe kapolo wabwino! Chifukwa wasonyeza kukhulupirika pa chinthu chaching’ono, ndakupatsa ulamuliro woyang’anira mizinda 10.’+
21 Mbuye wakeyo anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe!+ Unakhulupirika+ pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti udziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’
17 Iye anamuuza kuti, ‘Unagwira ntchito, ndiwe kapolo wabwino! Chifukwa wasonyeza kukhulupirika pa chinthu chaching’ono, ndakupatsa ulamuliro woyang’anira mizinda 10.’+