Yohane 12:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Komanso ndikudziwa kuti lamulo lake limatanthauza moyo wosatha.+ Choncho zimene ndimalankhula, monga mmene Atate anandiuzira, ndimazilankhula momwemo.”+ Chivumbulutso 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anavala malaya akunja owazidwa magazi,+ ndipo dzina limene anali kutchedwa nalo linali lakuti Mawu+ a Mulungu.
50 Komanso ndikudziwa kuti lamulo lake limatanthauza moyo wosatha.+ Choncho zimene ndimalankhula, monga mmene Atate anandiuzira, ndimazilankhula momwemo.”+
13 Iye anavala malaya akunja owazidwa magazi,+ ndipo dzina limene anali kutchedwa nalo linali lakuti Mawu+ a Mulungu.