Yohane 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”
10 Pamenepo Pilato anati: “Kodi sukundilankhula?+ Kodi sukudziwa kuti ine ndili ndi mphamvu yokumasula, komanso yokupachika?”