Yohane 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndakulemekezani+ padziko lapansi, popeza ndatsiriza kugwira ntchito imene munandipatsa.+