-
Yohane 20:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Anaonanso nsalu ina imene anamukulungira kumutu ataipindapinda ndi kuiika payokha. Imeneyi sinaikidwe pamodzi ndi nsalu zokulungira mtembozo.
-