Yohane 11:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Amene anali wakufa uja anatuluka. Mapazi ndi manja ake anali okulungidwa ndi nsalu zamaliro,+ nkhope yakenso inali yomanga ndi nsalu. Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “M’masuleni ndi kumuleka apite.”
44 Amene anali wakufa uja anatuluka. Mapazi ndi manja ake anali okulungidwa ndi nsalu zamaliro,+ nkhope yakenso inali yomanga ndi nsalu. Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “M’masuleni ndi kumuleka apite.”