Yohane 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Makolo akewo ananena zimenezi chifukwa anali kuopa+ atsogoleri achipembedzo achiyuda. Pakuti iwo anali atagwirizana kale kuti, ngati wina angavomereze kuti Yesu alidi Khristu, adzamuchotsa musunagoge.+
22 Makolo akewo ananena zimenezi chifukwa anali kuopa+ atsogoleri achipembedzo achiyuda. Pakuti iwo anali atagwirizana kale kuti, ngati wina angavomereze kuti Yesu alidi Khristu, adzamuchotsa musunagoge.+