Yohane 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mmodzi wa ophunzira ake amene Yesu anali kumukonda,+ anakhala patsogolo pa Yesu, pachifuwa chake. Yohane 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo iye anathamanga ndi kukafika kwa Simoni Petulo ndi kwa wophunzira wina,+ amene Yesu anali kumukonda kwambiri uja. Iye anawauza kuti: “Ambuye awachotsa m’manda achikumbutso+ aja, ndipo sitikudziwa kumene awaika.”
2 Pamenepo iye anathamanga ndi kukafika kwa Simoni Petulo ndi kwa wophunzira wina,+ amene Yesu anali kumukonda kwambiri uja. Iye anawauza kuti: “Ambuye awachotsa m’manda achikumbutso+ aja, ndipo sitikudziwa kumene awaika.”