Machitidwe 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipotu Davide sanakwere kumwamba,+ koma iye mwini anati, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+ Aheberi 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero mzimu woyera ukuonetsa poyera kuti njira+ yolowera kumalo oyera amkatikati inali isanaonekere pamene chihema choyambacho chinalipo.+
34 Ndipotu Davide sanakwere kumwamba,+ koma iye mwini anati, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+
8 Chotero mzimu woyera ukuonetsa poyera kuti njira+ yolowera kumalo oyera amkatikati inali isanaonekere pamene chihema choyambacho chinalipo.+