1 Yohane 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi chimenechi chikutanthauza kuti ife sitinakonde Mulungu, koma iye ndi amene anatikonda ndi kutumiza Mwana wake monga nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ 1 Yohane 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ife timasonyeza chikondi, chifukwa iye ndi amene anayamba kutikonda.+
10 Chikondi chimenechi chikutanthauza kuti ife sitinakonde Mulungu, koma iye ndi amene anatikonda ndi kutumiza Mwana wake monga nsembe+ yophimba+ machimo athu.+