Yohane 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwalako kukuunika mumdima,+ ndipo mdimawo sunagonjetse kuwalako.