Mateyu 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anali kuwabatiza mumtsinje wa Yorodano,+ ndipo anthuwo anali kuulula machimo awo poyera.