Yohane 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yesu anawayankha kuti: “Zimene ine ndimaphunzitsa si zanga ayi, koma ndi za amene anandituma.+