Yohane 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atatewo amakonda Mwana wake.+ Amamuonetsa zonse zimene iwo akuchita, ndipo adzamuonetsa ntchito zazikulu kuposa izi, kuti inu mudabwe.+ Yohane 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Monga Atate wakondera ine,+ inenso kukonda inu, inunso khalanibe m’chikondi changa.
20 Atatewo amakonda Mwana wake.+ Amamuonetsa zonse zimene iwo akuchita, ndipo adzamuonetsa ntchito zazikulu kuposa izi, kuti inu mudabwe.+