Yohane 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti monga Atate ali nawo moyo mwa iwo wokha,+ alolanso Mwana kukhala nawo moyo mwa iye yekha.+ 1 Akorinto 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti monga mwa Adamu onse akufa,+ momwemonso mwa Khristu onse adzapatsidwa+ moyo.