Yohane 5:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Sindikufuna ulemerero wochokera kwa anthu,+ Yohane 8:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Komatu ine sindikudzifunira ndekha ulemerero.+ Alipo Wina amene akuufuna ndipo iye ndi woweruza.+