Genesis 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako Mulungu anati: “Tiyeni+ tipange munthu m’chifaniziro chathu,+ kuti akhale wofanana nafe.+ Ayang’anire nsomba zam’nyanja ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga, komanso nyama zoweta. Ayang’anirenso dziko lonse lapansi ndi nyama zonse zokwawa padziko lapansi.”+ Genesis 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Yehova Mulungu anati: “Tsopano munthu wakhala wodziwa zabwino ndi zoipa ngati ife.+ Choncho, kuti asathyolenso ndi kudya chipatso cha mtengo wa moyo,+ n’kukhala ndi moyo mpaka kalekale,* . . .”
26 Kenako Mulungu anati: “Tiyeni+ tipange munthu m’chifaniziro chathu,+ kuti akhale wofanana nafe.+ Ayang’anire nsomba zam’nyanja ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga, komanso nyama zoweta. Ayang’anirenso dziko lonse lapansi ndi nyama zonse zokwawa padziko lapansi.”+
22 Ndiyeno Yehova Mulungu anati: “Tsopano munthu wakhala wodziwa zabwino ndi zoipa ngati ife.+ Choncho, kuti asathyolenso ndi kudya chipatso cha mtengo wa moyo,+ n’kukhala ndi moyo mpaka kalekale,* . . .”