Maliko 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi iyeyu si mmisiri wamatabwa,+ mwana wa Mariya,+ komanso m’bale wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo alongo ake si awa omwe tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Yohane 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Poyankha Yesu anati: “Ngakhale kuti ndimadzichitira ndekha umboni,+ umboni wanga ndi woona, chifukwa ndikudziwa kumene ndinachokera ndi kumene ndikupita.+ Koma inu simukudziwa kumene ndinachokera ndi kumene ndikupita.
3 Kodi iyeyu si mmisiri wamatabwa,+ mwana wa Mariya,+ komanso m’bale wake wa Yakobo,+ Yosefe, Yudasi ndi Simoni?+ Ndipo alongo ake si awa omwe tili nawo pompano?” Choncho anayamba kukhumudwa naye.+
14 Poyankha Yesu anati: “Ngakhale kuti ndimadzichitira ndekha umboni,+ umboni wanga ndi woona, chifukwa ndikudziwa kumene ndinachokera ndi kumene ndikupita.+ Koma inu simukudziwa kumene ndinachokera ndi kumene ndikupita.