Deuteronomo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati panu, kuchokera pakati pa abale anu, ndipo inu mudzamvere mneneri ameneyo.+ Yohane 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano anthuwo ataona zizindikiro zimene anachitazo, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri+ uja amene anati adzabwera padziko.” Yohane 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho ena m’khamulo, amene anamva mawu amenewa, anayamba kunena kuti: “Ameneyu ndi Mneneri ndithu.”+ Machitidwe 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipotu Mose ananena kuti, ‘Yehova Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu.+ Mudzamumvere pa zinthu zonse zimene adzakuuzeni.+
15 Yehova Mulungu wanu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati panu, kuchokera pakati pa abale anu, ndipo inu mudzamvere mneneri ameneyo.+
14 Tsopano anthuwo ataona zizindikiro zimene anachitazo, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri+ uja amene anati adzabwera padziko.”
40 Choncho ena m’khamulo, amene anamva mawu amenewa, anayamba kunena kuti: “Ameneyu ndi Mneneri ndithu.”+
22 Ndipotu Mose ananena kuti, ‘Yehova Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine kuchokera pakati pa abale anu.+ Mudzamumvere pa zinthu zonse zimene adzakuuzeni.+