Genesis 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, ndipo mayiko onsewa ndidzawapereka kwa mbewu yako.+ Mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso*+ ndithu kudzera mwa mbewu yako.’ Mateyu 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi. Yohane 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu ndife ana a Abulahamu+ ndipo sitinakhalepo akapolo a munthu.+ Tsopano iwe ukunena bwanji kuti, ‘Mudzamasulidwa’?”
4 ‘Ndidzachulukitsa mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, ndipo mayiko onsewa ndidzawapereka kwa mbewu yako.+ Mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso*+ ndithu kudzera mwa mbewu yako.’
9 Musamadzinyenge kuti, ‘Tili ndi atate wathu Abulahamu.’+ Pakuti ndikukuuzani kuti Mulungu angathe kuutsira Abulahamu+ ana kuchokera kumiyala iyi.
33 Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu ndife ana a Abulahamu+ ndipo sitinakhalepo akapolo a munthu.+ Tsopano iwe ukunena bwanji kuti, ‘Mudzamasulidwa’?”