Yohane 12:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ngati munthu wamva mawu anga koma osawasunga, ine sindiweruza woteroyo, pakuti sindinabwere kudzaweruza dziko,+ koma kudzalipulumutsa.+
47 Ngati munthu wamva mawu anga koma osawasunga, ine sindiweruza woteroyo, pakuti sindinabwere kudzaweruza dziko,+ koma kudzalipulumutsa.+