Yohane 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+ Yohane 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mwamupatsa ulamuliro pa anthu onse,+ kuti onse amene inu mwamupatsa,+ awapatse moyo wosatha.+
24 Ndithudi ndikukuuzani, Iye wakumva mawu anga ndi kukhulupirira amene anandituma ine ali nawo moyo wosatha,+ ndipo salowa m’chiweruzo koma wachoka ku imfa, waolokera ku moyo.+