Yohane 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+
10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+