Yohane 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepa anali kunena za mzimu umene onse okhulupirira mwa iye anali pafupi kulandira. Pakuti pa nthawiyi n’kuti asanaulandire,+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+
39 Pamenepa anali kunena za mzimu umene onse okhulupirira mwa iye anali pafupi kulandira. Pakuti pa nthawiyi n’kuti asanaulandire,+ chifukwa Yesu anali asanalandire ulemerero wake.+