Yohane 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiponso, monga mmene Mose anakwezera njoka m’mwamba+ m’chipululu, momwemonso Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa m’mwamba,+ Yohane 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anali asanazindikire malemba akuti Yesu ayenera kuuka kwa akufa.+
14 Ndiponso, monga mmene Mose anakwezera njoka m’mwamba+ m’chipululu, momwemonso Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa m’mwamba,+