Deuteronomo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamula.+ Yohane 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Zimene ndinaziona kwa Atate wanga+ ndi zimene ndimalankhula.+ Chotero inunso mumachita zimene mwamva kwa atate wanu.” Yohane 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+
18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamula.+
38 Zimene ndinaziona kwa Atate wanga+ ndi zimene ndimalankhula.+ Chotero inunso mumachita zimene mwamva kwa atate wanu.”
10 Sukukhulupirira kodi, kuti Atate ndi ine ndife ogwirizana?+ Zinthu zimene ine ndimanena kwa inu sindilankhula za m’maganizo mwanga, koma Atate amene ali wogwirizana ndi ine ndiye akuchita ntchito zake.+