Yohane 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuyambira tsopano ndikukuuziranitu zisanachitike,+ kuti zikadzachitika mudzakhulupirire kuti ine ndinedi amene munali kumuyembekezera uja. Yohane 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho, ndakuuzani zisanachitike,+ kuti zikachitika, mukhulupirire.
19 Kuyambira tsopano ndikukuuziranitu zisanachitike,+ kuti zikadzachitika mudzakhulupirire kuti ine ndinedi amene munali kumuyembekezera uja.