Yohane 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo Yesu anati: “Ndikhala nanube kanthawi pang’ono ndisanapite kwa iye amene anandituma.+ Yohane 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yesu anali kudziwa kuti Atate anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+ Analinso kudziwa kuti anabwera kuchokera kwa Mulungu ndi kuti anali kupita kwa Mulungu.+
3 Yesu anali kudziwa kuti Atate anapereka zinthu zonse m’manja mwake.+ Analinso kudziwa kuti anabwera kuchokera kwa Mulungu ndi kuti anali kupita kwa Mulungu.+