Yohane 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano dziko ili likuweruzidwa, wolamulira wa dzikoli+ aponyedwa kunja tsopano.+ Yohane 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Sindilankhula nanunso zambiri, pakuti wolamulira+ wa dziko akubwera. Iye alibe mphamvu pa ine,+