Yohane 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yesu anawayankha kuti: “Nthawi yafika yakuti Mwana wa munthu alemekezedwe.+ Yohane 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mulungunso payekha amulemekeza iye,+ ndipo amulemekeza nthawi yomwe ino.