Aefeso 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kufikira tonse tidzafike pa umodzi m’chikhulupiriro komanso pa kumudziwa molondola Mwana wa Mulungu, inde, kufikira tidzakhale munthu wachikulire,+ wofika pa msinkhu wauchikulire umene Khristu anafikapo.+ Afilipi 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirire kukula,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola,+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+ 1 Timoteyo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithu Timoteyo, sunga bwino chimene chinaikidwa m’manja mwako.+ Pewa nkhani zopanda pake zimene zimaipitsa zinthu zoyera. Upewenso mitsutso pa zimene ena monama amati ndiye “kudziwa zinthu.”+ 2 Petulo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu musatero ayi, koma pitirizani kulandira kukoma mtima kwakukulu ndi kumudziwa Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu.+ Kwa iye kukhale ulemerero, kuyambira panopa mpaka muyaya.+
13 kufikira tonse tidzafike pa umodzi m’chikhulupiriro komanso pa kumudziwa molondola Mwana wa Mulungu, inde, kufikira tidzakhale munthu wachikulire,+ wofika pa msinkhu wauchikulire umene Khristu anafikapo.+
9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirire kukula,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola,+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+
20 Ndithu Timoteyo, sunga bwino chimene chinaikidwa m’manja mwako.+ Pewa nkhani zopanda pake zimene zimaipitsa zinthu zoyera. Upewenso mitsutso pa zimene ena monama amati ndiye “kudziwa zinthu.”+
18 Ndithu musatero ayi, koma pitirizani kulandira kukoma mtima kwakukulu ndi kumudziwa Ambuye ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu.+ Kwa iye kukhale ulemerero, kuyambira panopa mpaka muyaya.+