Yohane 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pambuyo pa zonsezi, kunali chikondwerero+ cha Ayuda, ndipo Yesu ananyamuka kupita ku Yerusalemu.