Luka 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inenso, popeza kuti ndafufuza zinthu zonse mosamala kwambiri kuchokera pa chiyambi, ndafunitsitsa kuti ndikulembereni mwatsatanetsatane,+ inu wolemekezeka+ koposa, a Teofilo.+
3 Inenso, popeza kuti ndafufuza zinthu zonse mosamala kwambiri kuchokera pa chiyambi, ndafunitsitsa kuti ndikulembereni mwatsatanetsatane,+ inu wolemekezeka+ koposa, a Teofilo.+