Machitidwe 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno pamene tinali kupita kumalo opempherera, tinakumana ndi mtsikana wina wantchito wogwidwa ndi mzimu,+ chiwanda cholosera zam’tsogolo.+ Iye anali kupezera mabwana ake phindu lochuluka+ mwa kumachita zoloserazo.
16 Ndiyeno pamene tinali kupita kumalo opempherera, tinakumana ndi mtsikana wina wantchito wogwidwa ndi mzimu,+ chiwanda cholosera zam’tsogolo.+ Iye anali kupezera mabwana ake phindu lochuluka+ mwa kumachita zoloserazo.