Mateyu 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+ Machitidwe 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti sindinakubisireni kanthu, koma ndinakuuzani chifuniro+ chonse cha Mulungu. 2 Timoteyo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 lalikira mawu.+ Lalikira modzipereka, m’nthawi yabwino+ ndi m’nthawi yovuta.+ Dzudzula,+ tsutsa, dandaulira. Chita zimenezi ndi luso la kuphunzitsa ndiponso moleza mtima kwambiri.+
20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+
2 lalikira mawu.+ Lalikira modzipereka, m’nthawi yabwino+ ndi m’nthawi yovuta.+ Dzudzula,+ tsutsa, dandaulira. Chita zimenezi ndi luso la kuphunzitsa ndiponso moleza mtima kwambiri.+