2 Akorinto 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza tili ndi utumiki umenewu+ malinga ndi chifundo chimene tinasonyezedwa,+ sitikubwerera m’mbuyo. 2 Akorinto 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma zinthu zonse n’zochokera kwa Mulungu, amene anatigwirizanitsa+ ndi iyeyo kudzera mwa Khristu, ndipo anatipatsa utumiki+ wokhazikitsanso mtendere.
4 Popeza tili ndi utumiki umenewu+ malinga ndi chifundo chimene tinasonyezedwa,+ sitikubwerera m’mbuyo.
18 Koma zinthu zonse n’zochokera kwa Mulungu, amene anatigwirizanitsa+ ndi iyeyo kudzera mwa Khristu, ndipo anatipatsa utumiki+ wokhazikitsanso mtendere.