Machitidwe 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’malomwake, anatsanzikana+ nawo ndi kuwauza kuti: “Yehova akalola ndidzabweranso kudzakuonani.”+ Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wa panyanja
21 M’malomwake, anatsanzikana+ nawo ndi kuwauza kuti: “Yehova akalola ndidzabweranso kudzakuonani.”+ Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wa panyanja