Mateyu 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Petulo anamutengera pambali ndi kuyamba kum’dzudzula kuti: “Dzikomereni mtima Ambuye. Musalole kuti zimenezi zikuchitikireni ngakhale pang’ono.”+
22 Kenako Petulo anamutengera pambali ndi kuyamba kum’dzudzula kuti: “Dzikomereni mtima Ambuye. Musalole kuti zimenezi zikuchitikireni ngakhale pang’ono.”+