Machitidwe 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso usiku, Ambuye anauza Paulo+ m’masomphenya kuti: “Usaope, pitiriza kulankhula. Usakhale chete, Machitidwe 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndi kunena kuti, ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara,+ ndipo taona! Chifukwa cha iwe, Mulungu mokoma mtima adzapulumutsa onse amene uli nawo pa ulendowu.’
9 Komanso usiku, Ambuye anauza Paulo+ m’masomphenya kuti: “Usaope, pitiriza kulankhula. Usakhale chete,
24 ndi kunena kuti, ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara,+ ndipo taona! Chifukwa cha iwe, Mulungu mokoma mtima adzapulumutsa onse amene uli nawo pa ulendowu.’